-
Yoswa 18:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Kumʼmawa, malire ake anali mtsinje wa Yorodano. Ichi chinali cholowa cha ana a Benjamini motsatira mabanja awo, ndi malire ake kuzungulira gawo lonse.
-
-
1 Mafumu 1:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako Adoniya anapereka nsembe+ za nkhosa, ngʼombe komanso ana a ngʼombe onenepa pafupi ndi mwala wa Zoheleti womwe uli pafupi ndi Eni-rogeli. Anaitana azichimwene ake onse omwe anali ana a mfumu komanso amuna onse a mu Yuda omwe anali atumiki a mfumu.
-