-
2 Samueli 19:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako Simeyi+ mwana wa Gera wa ku Bahurimu, wa fuko la Benjamini, anathamangira amuna a ku Yuda nʼkupita nawo kukakumana ndi Mfumu Davide.
-