-
1 Samueli 19:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Nthawi yomweyo, Mikala anathandiza Davide kuti atulukire pawindo nʼkuthawa.
-
-
1 Samueli 19:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Sauli anatuma anthu kuti akamutenge Davide, koma Mikala anawauza kuti: “Wadwala.”
-
-
1 Samueli 21:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Davide anayankha Ahimeleki wansembe kuti: “Mfumu yandituma kuti ndikachite zinazake ndipo yandiuza kuti, ‘Usauze aliyense zimene ndakutumazi komanso malangizo amene ndakupatsa.’ Ndapangana ndi anyamata anga kuti ndikumane nawo penapake.
-