-
1 Mafumu 16:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Zimiri ataona kuti mzindawo walandidwa, anakalowa munsanja yomwe inali panyumba ya mfumu nʼkuyatsa nyumbayo iye ali momwemo, moti anafa.+
-
-
Salimo 5:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma Mulungu adzawapeza ndi mlandu.
Adzagwa chifukwa cha ziwembu zawo zomwe.+
Muwathamangitse chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zawo,
Chifukwa iwo akupandukirani.
-