-
Deuteronomo 3:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ogi mfumu ya ku Basana ndi amene anali womaliza pa Arefai amene anatsala. Chithatha chimene* anaikapo mtembo wake chinali chachitsulo ndipo mpaka pano chidakali ku Raba wa Aamoni. Mulitali mwake nʼchokwana masentimita 401,* ndipo mulifupi mwake masentimita 178,* potengera muyezo umene unakhazikitsidwa.
-
-
2 Samueli 12:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Choncho Davide anasonkhanitsa asilikali onse nʼkupita ku Raba ndipo anamenyana ndi anthu amumzindawo nʼkuulanda.
-