-
2 Samueli 16:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno mfumu inafunsa Ziba kuti: “Nʼchifukwa chiyani wabweretsa zinthu zimenezi?” Ziba anayankha kuti: “Abuluwa ndatengera anthu amʼnyumba ya mfumu kuti azikwerapo, mikate ndi makeke a zipatso zamʼchilimwezi ndatengera anyamata kuti adye ndipo vinyoyu ndatenga kuti anthu amene atopa mʼchipululu, azimwa.”+
-