Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Ekisodo 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 35:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Aliyense amene wapha munthu aziphedwa+ pambuyo poti mboni zatsimikizira.+ Koma munthu sakuyenera kuphedwa ngati pali umboni woperekedwa ndi munthu mmodzi yekha. Numeri 35:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musamadetse dziko limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndi amene amadetsa dziko.+ Ndipo dziko limene ladetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe ndi china chilichonse, kupatulapo magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+
30 Aliyense amene wapha munthu aziphedwa+ pambuyo poti mboni zatsimikizira.+ Koma munthu sakuyenera kuphedwa ngati pali umboni woperekedwa ndi munthu mmodzi yekha.
33 Musamadetse dziko limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndi amene amadetsa dziko.+ Ndipo dziko limene ladetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe ndi china chilichonse, kupatulapo magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+