-
1 Samueli 9:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Munthu amene ndinakuuza uja ndi ameneyu. Uja ndinati, ‘Ndi amene adzalamulire anthu anga.’”+
-