Deuteronomo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Arefai+ nawonso ankaoneka ngati Aanaki,+ ndipo Amowabu ankawatchula kuti Aemi.