Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Samueli 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi,* dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali pafupifupi mamita atatu.*

  • 1 Samueli 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu,+ ndipo mutu wachitsulo wa mkondowo unali wolemera makilogalamu pafupifupi 7.* Munthu womunyamulira chishango chake ankayenda patsogolo pake.

  • 1 Mbiri 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Benaya anaphanso munthu wamkulu modabwitsa wa ku Iguputo, yemwe anali wamtali mikono 5.*+ Ngakhale kuti munthuyu anali ndi mkondo mʼmanja mwake, waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu,+ Benaya anapita kukakumana naye atanyamula ndodo ndipo analanda mkondowo nʼkumupha ndi mkondo wake womwewo.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani