1 Samueli 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi,* dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali pafupifupi mamita atatu.* 1 Samueli 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu,+ ndipo mutu wachitsulo wa mkondowo unali wolemera makilogalamu pafupifupi 7.* Munthu womunyamulira chishango chake ankayenda patsogolo pake.
4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi,* dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali pafupifupi mamita atatu.*
7 Mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu,+ ndipo mutu wachitsulo wa mkondowo unali wolemera makilogalamu pafupifupi 7.* Munthu womunyamulira chishango chake ankayenda patsogolo pake.