1 Samueli 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Samueli 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana atatu aakulu a Jese anapita ndi Sauli kunkhondo.+ Woyamba kubadwa dzina lake anali Eliyabu,+ wachiwiri anali Abinadabu+ ndipo wachitatu anali Shama.+ 1 Mbiri 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Jese anabereka mwana wake woyamba Eliyabu, wachiwiri Abinadabu,+ wachitatu Simeya,+
13 Ana atatu aakulu a Jese anapita ndi Sauli kunkhondo.+ Woyamba kubadwa dzina lake anali Eliyabu,+ wachiwiri anali Abinadabu+ ndipo wachitatu anali Shama.+