-
2 Samueli 2:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Koma Asaheli sanasiye kumuthamangitsa. Choncho Abineri anamubaya pamimba ndi chogwirira cha mkondo+ ndipo mkondowo unatulukira kumsana moti anagwa pansi nʼkufera pomwepo. Aliyense akafika pamalo amene Asaheli anafera, ankaima kaye.
-