-
2 Samueli 23:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Abisai,+ mchimwene wake wa Yowabu mwana wa Zeruya+ anali mtsogoleri wa anthu ena atatu. Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300. Abisai anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+ 19 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kwambiri kuposa amuna ena atatuwo, ndipo anali mtsogoleri wawo, iye sankafanana ndi amuna atatu oyambirira aja.
-