-
Levitiko 4:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ngʼombeyo azichita nayo ngati mmene anachitira ndi ngʼombe ina ya nsembe yamachimo ija. Azichita zomwezo, ndipo wansembe aziwaphimbira machimo awo+ ndipo adzakhululukidwa.
-
-
2 Mbiri 29:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Kenako ansembe anazipha nʼkuzipereka nsembe yamachimo ndipo anaika magazi ake paguwa lansembe kuti aphimbe machimo a Aisiraeli onse, popeza mfumu inanena kuti nsembe yopsereza ndi yamachimoyo ikhale ya Aisiraeli onse.
-