-
1 Samueli 24:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzaona nkhaniyi nʼkundiweruza kuti ndine wosalakwa+ ndipo adzandipulumutsa mʼmanja mwanu.”
-