2 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Davide anafunsa Yehova kuti:+ “Kodi ndipite mumzinda wina wa Yuda?” Yehova anamuyankha kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+ 2 Samueli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, mafuko onse a Isiraeli anapita kwa Davide ku Heburoni+ nʼkumuuza kuti: “Ife ndi inu ndife magazi amodzi.*+
2 Kenako Davide anafunsa Yehova kuti:+ “Kodi ndipite mumzinda wina wa Yuda?” Yehova anamuyankha kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+
5 Patapita nthawi, mafuko onse a Isiraeli anapita kwa Davide ku Heburoni+ nʼkumuuza kuti: “Ife ndi inu ndife magazi amodzi.*+