-
2 Samueli 8:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki mwana wa Abiyatara anali ansembe, ndipo Seraya anali mlembi.
-
-
1 Mbiri 27:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Atsogoleri a mafuko a Isiraeli anali awa: Mtsogoleri wa fuko la Rubeni anali Eliezere mwana wa Zikiri, wa fuko la Simiyoni anali Sefatiya mwana wa Maaka, 17 wa fuko la Levi anali Hasabiya mwana wa Kemueli, wa ana a Aroni anali Zadoki,
-