Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mbiri 8:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mwana woyamba wa Benjamini+ anali Bela,+ wachiwiri anali Asibeli,+ wachitatu anali Ahara,

  • 1 Mbiri 8:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Nera+ anabereka Kisi, Kisi anabereka Sauli,+ Sauli anabereka Yonatani,+ Malikisuwa,+ Abinadabu+ ndi Esibaala.*+

  • 1 Mbiri 12:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Awa ndi anthu amene anapita kwa Davide ku Zikilaga+ pa nthawi imene iye sankayenda momasuka chifukwa choopa Sauli+ mwana wa Kisi. Iwowa anali ena mwa asilikali amphamvu amene anamuthandiza pankhondo.+ 2 Amuna amenewa anali onyamula mauta ndipo ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ poponya miyala ndi gulaye+ kapena poponya mivi ndi uta. Amenewa anali abale ake a Sauli, a fuko la Benjamini.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani