-
1 Mbiri 14:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Davide anatchuka mpaka mbiri yake inamveka kumayiko onse ndipo Yehova anachititsa kuti anthu a mitundu yonse azimuopa Davideyo.+
-
-
Salimo 18:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Anthu akadzangomva mphekesera zokhudza ine, adzandimvera.
Anthu ochokera mʼdziko lina adzandigwadira mwamantha.+
-