-
1 Mafumu 7:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Kenako anapanga zotengera 10+ zakopa zokhala ndi mawilo. Chotengera chilichonse chinali mikono 4 mulitali, mikono 4 mulifupi komanso mikono itatu kupita mʼmwamba.
-
-
1 Mafumu 7:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Kenako anapanga mabeseni 10 akopa.+ Mʼbeseni lililonse munkalowa madzi okwana mitsuko 40, ndipo linali mikono 4 kuchokera mbali ina kufika mbali ina. Pa zotengera 10 zija, chilichonse chinali ndi beseni lake.
-