-
1 Mafumu 7:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Solomo sanayeze kulemera kwa ziwiya zonse chifukwa zinali zambiri. Kopayo sanadziwike kulemera kwake.+
-
-
Yeremiya 52:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma zinali zosatheka kuyeza kulemera kwa kopa wa zipilala ziwiri zija, thanki yosungira madzi, ngʼombe zakopa 12+ zimene zinali pansi pa thanki yosungira madzi ndiponso zotengera zokhala ndi mawilo zimene Mfumu Solomo anapanga kuti zizigwira ntchito panyumba ya Yehova chifukwa anali wochuluka kwambiri.
-