-
1 Mafumu 6:31, 32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Pakhomo la chipinda chamkati anaikapo zitseko za mtengo wa paini, zipilala zamʼmbali ndiponso mafelemu, ngati mbali ya 5. 32 Zitseko ziwirizo zinali zamatabwa a mtengo wa paini ndipo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mitengo ya kanjedza ndi maluwa. Zitsekozo anazikuta ndi golide. Akerubi ndi mitengo ya kanjedza zomwe anazilemba mochita kugoba pazitsekozo anazikutanso ndi golide.
-