Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 6:33-35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Anapanganso chimodzimodzi ndi khomo la kachisi,* pamafelemu ake a mtengo wa paini omwe anali mbali ya 4. 34 Anapanga zitseko ziwiri zamatabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza. Chitseko choyamba chinali ndi mbali ziwiri ndipo hafu inkatsegukira mbali ina, hafu ina inkatsegukira mbali ina. Chitseko chachiwiri chinalinso ndi mbali ziwiri ndipo hafu inkatsegukira mbali ina, hafu ina inkatsegukira mbali ina.+ 35 Pazitsekopo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mitengo ya kanjedza komanso maluwa ndipo anakuta zojambulazo ndi golide.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani