-
1 Mafumu 7:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mfumu Solomo anatuma anthu kuti akatenge Hiramu+ ku Turo. 14 Mayi ake anali mkazi wamasiye wa fuko la Nafitali. Bambo ake anali a ku Turo odziwa kupanga zinthu zakopa.*+ Hiramu anali waluso, womvetsa zinthu+ ndiponso wodziwa bwino ntchito yopanga zinthu zakopa. Iye anabwera kwa Mfumu Solomo ndipo anamugwirira ntchito yake yonse.
-