-
1 Mafumu 15:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo anatsatira chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake, kupatulapo pa nkhani ya Uriya Muhiti.+
-