-
1 Mafumu 6:33, 34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Anapanganso chimodzimodzi ndi khomo la kachisi,* pamafelemu ake a mtengo wa paini omwe anali mbali ya 4. 34 Anapanga zitseko ziwiri zamatabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza. Chitseko choyamba chinali ndi mbali ziwiri ndipo hafu inkatsegukira mbali ina, hafu ina inkatsegukira mbali ina. Chitseko chachiwiri chinalinso ndi mbali ziwiri ndipo hafu inkatsegukira mbali ina, hafu ina inkatsegukira mbali ina.+
-