Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mbiri 15:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Komanso Davide anaitanitsa Zadoki+ ndi Abiyatara,+ omwe anali ansembe. Anaitanitsanso Alevi awa: Uriyeli, Asaya, Yoweli, Semaya, Elieli ndi Aminadabu. 12 Ndiyeno anawauza kuti: “Inuyo ndinu atsogoleri a nyumba za makolo a Alevi. Choncho inu ndi abale anu mudziyeretse ndipo mukatenge Likasa la Yehova Mulungu wa Isiraeli nʼkukaliika kumalo amene ndakonza kuti lizikhalako.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani