Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 2:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Iwo amauza mtengo kuti, ‘Ndinu bambo anga,’+

      Ndipo mwala amauuza kuti, ‘Ndinu amene munandibereka.’

      Koma ine andifulatira ndipo sanandisonyeze nkhope yawo.+

      Koma tsoka likadzawagwera adzanena kuti,

      ‘Bwerani mudzatipulumutse!’+

  • Ezekieli 8:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Choncho anandipititsa kubwalo lamkati la nyumba ya Yehova.+ Ndiyeno ndinaona kuti pakhomo lolowera mʼkachisi wa Yehova, pakati pa khonde ndi guwa lansembe, panali amuna pafupifupi 25 atafulatira kachisi wa Yehova ndipo nkhope zawo zinali zitayangʼana kumʼmawa. Iwo ankagwadira dzuwa limene linali kumʼmawa.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani