Numeri 4:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Muwerenge ana onse a Kohati+ mwa ana a Levi, potengera mabanja awo komanso nyumba za makolo awo. 3 Muwerenge onse kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ amene ali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azigwira ntchito mʼchihema chokumanako.+ 1 Mbiri 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Kohati analipo 4: Amuramu, Izara,+ Heburoni ndi Uziyeli.+
2 “Muwerenge ana onse a Kohati+ mwa ana a Levi, potengera mabanja awo komanso nyumba za makolo awo. 3 Muwerenge onse kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ amene ali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azigwira ntchito mʼchihema chokumanako.+