Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mafumu 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako mfumuyo inalamula Hilikiya+ mkulu wa ansembe, ansembe ena ndiponso alonda apakhomo kuti atulutse mʼkachisi wa Yehova ziwiya zonse zimene anapangira Baala, mzati wopatulika*+ ndi gulu lonse la zinthu zakuthambo. Itatero, inakazitentha kunja kwa Yerusalemu pamalo otsetsereka a ku Kidironi ndipo phulusa lake inapita nalo ku Beteli.+

  • 2 Mafumu 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mfumuyo inatulutsa mzati* wopatulika+ umene unali mʼnyumba ya Yehova ndipo inapita nawo kuchigwa cha Kidironi kunja kwa mzinda wa Yerusalemu nʼkukautentha.+ Itatero, inauperapera nʼkuwaza fumbi lake pamanda a anthu wamba.+

  • 2 Mbiri 15:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yohane 18:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani