1 Mafumu 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Khonde+ lakutsogolo kwa kachisi* linali mikono 20 mulitali ndipo linkafanana ndi mulifupi mwa nyumbayo. Khondelo linali kutsogolo kwa nyumbayo ndipo linali mikono 10 mulifupi. 1 Mbiri 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu, zipinda zake zapadenga, zipinda zake zamkati ndiponso nyumba yokhalamo chivundikiro chophimbira machimo.+
3 Khonde+ lakutsogolo kwa kachisi* linali mikono 20 mulitali ndipo linkafanana ndi mulifupi mwa nyumbayo. Khondelo linali kutsogolo kwa nyumbayo ndipo linali mikono 10 mulifupi.
11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu, zipinda zake zapadenga, zipinda zake zamkati ndiponso nyumba yokhalamo chivundikiro chophimbira machimo.+