-
1 Mbiri 25:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ana onsewa ankayangʼaniridwa ndi bambo awo poimba nyimbo panyumba ya Yehova. Ankaimba nyimbozo ndi zinganga, zoimbira za zingwe ndi azeze,+ potumikira panyumba ya Mulungu woona.
Koma Asafu, Yedutuni ndi Hemani ankayangʼaniridwa ndi mfumu.
-