2 Samueli 24:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Davide atadzuka mʼmawa, Yehova anauza mneneri Gadi,+ wamasomphenya wa Davide, kuti: 12 “Pita, ukamuuze Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pali zilango zitatu zimene ndingakupatse ndipo iwe usankhepo chimodzi.”’”+ 1 Mbiri 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zokhudza Mfumu Davide, kuyambira pachiyambi mpaka kumapeto, zikupezeka mʼzinthu zimene analemba Samueli wamasomphenya,* mneneri Natani+ ndiponso Gadi+ wamasomphenya.
11 Davide atadzuka mʼmawa, Yehova anauza mneneri Gadi,+ wamasomphenya wa Davide, kuti: 12 “Pita, ukamuuze Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pali zilango zitatu zimene ndingakupatse ndipo iwe usankhepo chimodzi.”’”+
29 Nkhani zokhudza Mfumu Davide, kuyambira pachiyambi mpaka kumapeto, zikupezeka mʼzinthu zimene analemba Samueli wamasomphenya,* mneneri Natani+ ndiponso Gadi+ wamasomphenya.