2 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Samueli 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova anatuma Natani+ kwa Davide. Atafika+ anamuuza kuti: “Panali amuna awiri amene ankakhala mumzinda umodzi. Wina anali wolemera ndipo wina anali wosauka.
12 Yehova anatuma Natani+ kwa Davide. Atafika+ anamuuza kuti: “Panali amuna awiri amene ankakhala mumzinda umodzi. Wina anali wolemera ndipo wina anali wosauka.