-
1 Mbiri 15:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Sebaniya, Yosafati, Netaneli, Amasai, Zekariya, Benaya ndi Eliezere, omwe anali ansembe, ankaimba malipenga mokweza patsogolo pa Likasa la Mulungu woona.+ Obedi-edomu ndi Yehiya nawonso anali alonda apageti panyumba yomwe munkakhala Likasa.
-