Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Numeri 8:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndidzapereka Alevi kwa Aroni ndi ana ake monga operekedwa kuchokera mwa Aisiraeli. Aleviwo adzatumikira mʼmalo mwa Aisiraeli pachihema chokumanako,+ ndipo aziphimba machimo a Aisiraeli kuti mliri usagwe pakati pawo+ chifukwa Aisiraeliwo ayandikira malo oyera.”

  • 2 Mbiri 30:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pagululo panali anthu ambiri amene sanadziyeretse. Choncho Alevi ndi amene ankapha nyama za Pasika za anthu onse amene sanali oyera,+ kuti awayeretse kwa Yehova.

  • 2 Mbiri 35:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iwo atamaliza kukonzekera, ansembe anaimirira mʼmalo awo, komanso Alevi anali mʼmagulu awo+ mogwirizana ndi zimene mfumu inalamula. 11 Atatero anapha nyama ya Pasika+ ndipo ansembe anawaza paguwa lansembe magazi amene anapatsidwa.+ Pa nthawiyi nʼkuti Alevi akusenda nyamazo.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani