Ekisodo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Levitiko 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda zofufumitsa ndi kudya mkatewo mʼmalo oyera. Aziudyera mʼbwalo la chihema chokumanako.+
16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda zofufumitsa ndi kudya mkatewo mʼmalo oyera. Aziudyera mʼbwalo la chihema chokumanako.+