Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 7:40-46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Hiramu+ anapanganso mabeseni, mafosholo+ ndi mbale zolowa.+

      Choncho iye anamaliza ntchito yonse imene ankagwirira Mfumu Solomo yopanga zinthu zotsatirazi panyumba ya Yehova:+ 41 zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yooneka ngati mbale zolowa imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo ndi maukonde awiri+ okutira mitu iwiri imene inali pamwamba pa zipilalazo. 42 Anapanganso makangaza 400+ oika pamaukonde awiri aja ndipo panali mizere iwiri ya makangaza pa ukonde uliwonse. Makangazawo anali okutira mitu iwiri yooneka ngati mbale zolowa imene inali pazipilala ziwiri zija. 43 Anapanganso zotengera 10,+ mabeseni 10+ oika pazotengerazo, 44 thanki+ imodzi, ngʼombe zamphongo 12 zokhala pansi pa thankiyo, 45 ndowa, mafosholo, mbale zolowa ndi ziwiya zina zonse. Hiramu anapanga zinthu zimenezi ndi kopa wonyezimira kuti Mfumu Solomo aziike mʼnyumba ya Yehova. 46 Mfumuyo inaumba zinthu zimenezi mʼzikombole zadongo mʼchigawo cha Yorodano, pakati pa Sukoti ndi Zeretani.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani