-
1 Mafumu 7:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Pamutu wa chipilala chilichonse anaikapo maukonde opangidwa ndi matcheni opotanapotana.+ Pamutu wina anaikapo ukonde wopangidwa ndi matcheni 7 ndipo pamutu winawo anaikaponso ukonde wopangidwa ndi matcheni 7.
-