-
1 Mafumu 7:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mitu iwiriyo inali pamwamba pa zipilala komanso pamwamba pa malo ozungulira amene analumikizira maukonde aja. Kuzungulira mutu uliwonse, panali makangaza 200 amene anali mʼmizere.+
-