-
Salimo 69:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pamene ndinavala ziguduli,
Iwo anayamba kundinyoza.*
12 Anthu amene amakhala pageti la mzinda amandinena,
Ndipo anthu oledzera amanena za ine akamaimba nyimbo zawo.
-