-
Salimo 24:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndi ndani angakwere kuphiri la Yehova,+
Ndipo ndi ndani angaime mʼmalo ake opatulika?
-
-
Salimo 84:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Osangalala ndi anthu amene amapeza mphamvu kuchokera kwa inu,+
Amene mitima yawo imalakalaka misewu yaikulu yopita kunyumba yanu.
-
-
Salimo 84:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mphamvu zawo zidzapitiriza kuwonjezeka pamene akuyenda.+
Aliyense wa iwo amaonekera pamaso pa Mulungu mu Ziyoni.
-