Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Mlaliki 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Komanso munthu azidzaopa malo okwera ndipo azidzadera nkhawa zinthu zoopsa mumsewu. Mtengo wa amondi udzachita maluwa,+ chiwala chizidzayenda mochita kudzikoka ndipo zakudya sizidzakoma,* chifukwa munthu adzakhala akupita kunyumba yake yokhalitsa+ ndipo olira azidzangoyendayenda mumsewu.+

  • Mlaliki 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu* udzabwerera kwa Mulungu woona amene anaupereka.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani