Yobu 10:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndisanapite kumalo amene sindidzabwerako,+Kudziko lamdima wandiweyani,*+22 Kudziko lamdima waukulu,Dziko lamdima wandiweyani komanso lachisokonezo,Kumene ngakhale kuwala kumafanana ndi mdima.”
21 Ndisanapite kumalo amene sindidzabwerako,+Kudziko lamdima wandiweyani,*+22 Kudziko lamdima waukulu,Dziko lamdima wandiweyani komanso lachisokonezo,Kumene ngakhale kuwala kumafanana ndi mdima.”