Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yobu 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Masiku anga akuthamanga kuposa mashini owombera nsalu,+

      Atha mofulumira ndipo ine ndilibe chiyembekezo.+

  • Yobu 14:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Madzi amaperepesa miyala

      Ndipo mitsinje yake imakokolola dothi lapadziko lapansi.

      Inunso mwawononga chiyembekezo cha munthu.

  • Yobu 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Wandigumula mbali zonse mpaka ndatheratu.

      Chiyembekezo changa wachizula ngati mtengo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani