-
Salimo 109:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ana ake* aziyendayenda ndipo akhale opemphapempha.
Azichoka mʼmabwinja mmene akukhala, nʼkukafunafuna chakudya.
-
-
Danieli 4:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Inuyo adzakuthamangitsani pakati pa anthu ndipo muzidzakhala ndi nyama zakutchire. Muzidzadya udzu ngati ngʼombe ndipo muzidzanyowa ndi mame akumwamba.+ Ndiyeno padzadutsa+ nthawi zokwana 7+ mpaka mutadziwa kuti Mulungu Wamʼmwambamwamba ndi Wolamulira wa maufumu a anthu ndiponso kuti amapereka ulamuliro kwa aliyense amene akufuna kumupatsa.+
-