-
Salimo 69:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anthu amene amakhala pageti la mzinda amandinena,
Ndipo anthu oledzera amanena za ine akamaimba nyimbo zawo.
-
-
Maliro 3:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndakhala chinthu choseketsa kwa anthu onse ndipo amandiimba mʼnyimbo yawo nʼkumandinyoza tsiku lonse.
-