Yobu 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati ndili wolakwa, tsoka kwa ine! Ndipo ngakhale nditakhala wosalakwa, sindingadzutse mutu wanga,+Chifukwa ndili ndi manyazi kwambiri ndipo ndikuvutika.+
15 Ngati ndili wolakwa, tsoka kwa ine! Ndipo ngakhale nditakhala wosalakwa, sindingadzutse mutu wanga,+Chifukwa ndili ndi manyazi kwambiri ndipo ndikuvutika.+