-
Yobu 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Yobu anatenga phale loti azidzikandira ndipo ankakhala paphulusa.+
-
-
Yobu 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako anakhala pansi limodzi ndi Yobuyo kwa masiku 7 masana ndi usiku. Palibe amene analankhula naye chilichonse chifukwa anaona kuti ululu wake unali waukulu kwambiri.+
-
-
Yobu 7:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndikagona ndimafunsa kuti, ‘Kodi kucha nthawi yanji?’+
Usikuwo umatalika ndipo ndimangotembenukatembenuka mpaka mʼbandakucha.
-